Yoswa 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa Arubeni ndi kwa Agadi, kutsidya la kum’mawa kwa Yorodano.+ Yoswa 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Mose anagawira dziko fuko la ana a Gadi potsata mabanja awo.+
8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa Arubeni ndi kwa Agadi, kutsidya la kum’mawa kwa Yorodano.+