Deuteronomo 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Yobu 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinkasambitsa mapazi anga m’mafuta a mkaka,Ndiponso pamene miyala inkanditulutsira mitsinje ya mafuta.+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
13 Anapitiriza kumuyendetsa pamapiri a dziko lapansi,+Moti anadya zokolola za m’minda.+Anapitirizanso kumudyetsa uchi wochokera m’thanthwe,+Ndi mafuta ochokera m’mwala wa nsangalabwi.+ Yobu 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene ndinkasambitsa mapazi anga m’mafuta a mkaka,Ndiponso pamene miyala inkanditulutsira mitsinje ya mafuta.+
6 Pamene ndinkasambitsa mapazi anga m’mafuta a mkaka,Ndiponso pamene miyala inkanditulutsira mitsinje ya mafuta.+