Yesaya 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+ Hoseya 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndine amene ndinaphunzitsa Efuraimu kuyenda,+ amenenso ndinamunyamula m’manja mwanga+ koma iye sanavomereze kuti ndinamuchiritsa.+
11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+
3 Koma ine ndine amene ndinaphunzitsa Efuraimu kuyenda,+ amenenso ndinamunyamula m’manja mwanga+ koma iye sanavomereze kuti ndinamuchiritsa.+