Miyambo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+ Miyambo 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wosunga lamulo akusunga moyo wake.+ Wosasamala za njira zake adzaphedwa.+
23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+