Ekisodo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo Mulungu anayamba kulankhula mawu awa, kuti:+ Ekisodo 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mose anakhalabe m’phirimo ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Mawu Khumi,* pamiyala yosemayo.+ Deuteronomo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo analemba pamiyalayo mawu ofanana ndi oyamba aja,+ Mawu Khumi,*+ amene Yehova anakuuzani m’phiri kuchokera pakati pa moto,+ tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Atatero, Yehova anandipatsa miyalayo.
28 Choncho Mose anakhalabe m’phirimo ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Mawu Khumi,* pamiyala yosemayo.+
4 Pamenepo analemba pamiyalayo mawu ofanana ndi oyamba aja,+ Mawu Khumi,*+ amene Yehova anakuuzani m’phiri kuchokera pakati pa moto,+ tsiku limene munasonkhana kuphiri.+ Atatero, Yehova anandipatsa miyalayo.