Deuteronomo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Yehova anatilamula kuti tizitsatira malangizo onsewa,+ tiziopa Yehova Mulungu wathu ndi kupindula nthawi zonse,+ kuti tikhale ndi moyo monga mmene zilili lero.+ Yoswa 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzikonda Yehova Mulungu wanu,+ ndipo potero tetezani miyoyo yanu nthawi zonse.+
24 Choncho Yehova anatilamula kuti tizitsatira malangizo onsewa,+ tiziopa Yehova Mulungu wathu ndi kupindula nthawi zonse,+ kuti tikhale ndi moyo monga mmene zilili lero.+