Ekisodo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka m’dziko la Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+
7 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka m’dziko la Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+