Ekisodo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anthu onse anali kumva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa ndipo anali kuona kung’anima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva ndi kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaimabe patali.+ Aheberi 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti simunafike paphiri limene mungathe kulikhudza,+ loyaka moto,+ lokhala ndi mtambo wakuda, mdima wandiweyani komanso lowombedwa ndi mphepo yamkuntho.+
18 Ndiyeno anthu onse anali kumva mabingu ndi kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa ndipo anali kuona kung’anima kwa mphezi ndiponso phiri likufuka utsi. Anthuwo atamva ndi kuona zimenezi ananjenjemera ndipo anaimabe patali.+
18 Pakuti simunafike paphiri limene mungathe kulikhudza,+ loyaka moto,+ lokhala ndi mtambo wakuda, mdima wandiweyani komanso lowombedwa ndi mphepo yamkuntho.+