Deuteronomo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Deuteronomo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova Mulungu wanu adzachita mdulidwe wa mitima yanu+ ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti mukhale ndi moyo.+
13 “Ndiyeno mukadzamveradi malamulo anga+ amene ndikukupatsani lero, moti n’kukonda Yehova Mulungu wanu ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
6 Yehova Mulungu wanu adzachita mdulidwe wa mitima yanu+ ndi mitima ya ana anu,+ kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti mukhale ndi moyo.+