1 Mbiri 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu.
14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu.