Numeri 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo khamu lonselo linayamba kudandaula mofuula, ndipo anthuwo anachezera kulira+ usiku wonse. Numeri 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anafika ngakhale pouzana kuti: “Tiyeni tisankhe mtsogoleri, tibwerere ku Iguputo!”+ Salimo 106:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anayamba kunyansidwa ndi dziko losiririka,+Ndipo analibe chikhulupiriro m’mawu ake.+
14 Pamenepo khamu lonselo linayamba kudandaula mofuula, ndipo anthuwo anachezera kulira+ usiku wonse.