Ekisodo 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mose analowa mumtambomo ndi kukwera m’phirimo.+ Mose anakhala mmenemo masiku 40, usana ndi usiku.+
18 Kenako Mose analowa mumtambomo ndi kukwera m’phirimo.+ Mose anakhala mmenemo masiku 40, usana ndi usiku.+