Deuteronomo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu anali kukuwongolerani, ngati mmene bambo amawongolerera mwana wake.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu anali kukuwongolerani, ngati mmene bambo amawongolerera mwana wake.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+