Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero mwambo umenewu uzikukumbutsani zimene zinachitikazi ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu ndi pamphumi panu,+ kuti chilamulo cha Yehova chikhale pakamwa panu.+ Zizikhala choncho chifukwa Yehova anakutulutsani mu Iguputo ndi mphamvu ya dzanja lake.+

  • Ekisodo 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mwambo umenewu ukhale ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu ndi chomanga pamphumi panu,*+ chifukwa Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi mphamvu ya dzanja lake.”+

  • Deuteronomo 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Uziwamanga padzanja lako+ monga chizindikiro, ndipo azikhala ngati chomanga pamphumi pako,*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena