Levitiko 26:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+ Deuteronomo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.
46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+
5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.