Levitiko 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nyamayo ndi chala chake n’kuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe+ zopsereza.
30 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nyamayo ndi chala chake n’kuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe+ zopsereza.