Numeri 14:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mose atalankhula mawuwo kwa ana onse a Isiraeli, anthu onsewo anayamba kulira kwambiri.+