Numeri 14:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Komanso, iwo anadzuka m’mawa kwambiri kuti apite kudera lamapiri lija, ndipo anati: “Tiyeni! Ife tipita kumalo amene Yehova ananena, chifukwa tachimwa.”+
40 Komanso, iwo anadzuka m’mawa kwambiri kuti apite kudera lamapiri lija, ndipo anati: “Tiyeni! Ife tipita kumalo amene Yehova ananena, chifukwa tachimwa.”+