Numeri 33:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mukalande dzikolo n’kukhalamo, chifukwa ndidzalipereka ndithu kwa inu kuti likhale lanu.+ Salimo 135:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dziko lawo analipereka kukhala cholowa,+Cholowa cha anthu ake Aisiraeli.+