Numeri 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Popeza kuti Aamaleki ndi Akanani+ akukhala kuchigwa, mawa mutembenuke, munyamuke ulendo wolowera kuchipululu podzera njira yopita ku Nyanja Yofiira.”+ Deuteronomo 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma inu, sinthani njira ndipo muyambe kulowera kuchipululu, kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira.’+
25 Popeza kuti Aamaleki ndi Akanani+ akukhala kuchigwa, mawa mutembenuke, munyamuke ulendo wolowera kuchipululu podzera njira yopita ku Nyanja Yofiira.”+
40 Koma inu, sinthani njira ndipo muyambe kulowera kuchipululu, kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira.’+