Levitiko 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi. Deuteronomo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Samala kuti usagwidwe mumsampha wawo,+ pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso pako, kutinso usafufuze za milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inali kutumikira bwanji milungu yawo? Ndithudi inenso ndidzachita zomwezo.’
26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.
30 Samala kuti usagwidwe mumsampha wawo,+ pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso pako, kutinso usafufuze za milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inali kutumikira bwanji milungu yawo? Ndithudi inenso ndidzachita zomwezo.’