1 Mbiri 6:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Ana a Kohati amene anatsala anawapatsa mizinda yochokera ku banja la fuko lina ndi hafu ya fuko la Manase, atachita maere. Anawapatsa mizinda 10.+
61 Ana a Kohati amene anatsala anawapatsa mizinda yochokera ku banja la fuko lina ndi hafu ya fuko la Manase, atachita maere. Anawapatsa mizinda 10.+