Numeri 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mizinda yonse imene mukapatse Alevi ikakwane 48. Mizindayi mukawapatse limodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+
7 Mizinda yonse imene mukapatse Alevi ikakwane 48. Mizindayi mukawapatse limodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+