Yoswa 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ana a Isiraeli anatumiza+ Pinihasi+ mwana wa wansembe Eleazara, kwa ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase, ku Giliyadi.
13 Kenako ana a Isiraeli anatumiza+ Pinihasi+ mwana wa wansembe Eleazara, kwa ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase, ku Giliyadi.