Numeri 33:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mukalande dzikolo n’kukhalamo, chifukwa ndidzalipereka ndithu kwa inu kuti likhale lanu.+