Genesis 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano iyi ndi mbiri ya Tera. Tera anabereka Abulamu, Nahori ndi Harana. Harana anabereka Loti.+