Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.
26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.