Numeri 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+ Machitidwe 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa nthawi ya zaka pafupifupi 40,+ anapirira khalidwe lawo m’chipululu.
34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+