Deuteronomo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ 1 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma muziopa+ Yehova ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse m’choonadi.+ Kumbukirani zinthu zazikulu zimene Yehova wakuchitirani.+ Machitidwe 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.
12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
24 Koma muziopa+ Yehova ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse m’choonadi.+ Kumbukirani zinthu zazikulu zimene Yehova wakuchitirani.+
31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.