Yoswa 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’mamawa kutacha, Yoswa ndi ana a Isiraeli onse ananyamuka ku Sitimu.+ Anayenda mpaka kukafika kumtsinje wa Yorodano, kumene anagona usiku umenewo asanawoloke.
3 M’mamawa kutacha, Yoswa ndi ana a Isiraeli onse ananyamuka ku Sitimu.+ Anayenda mpaka kukafika kumtsinje wa Yorodano, kumene anagona usiku umenewo asanawoloke.