Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+