Deuteronomo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akazi anu okha ndi ana anu aang’ono ndiwo atsale m’mizinda yanu imene ndakupatsani.+ Ziweto zanunso zitsale (ndikudziwa kuti muli ndi ziweto zambiri), Deuteronomo 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako tinatenga dziko lawo ndi kulipereka monga cholowa kwa fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase.+ Yoswa 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa Arubeni ndi kwa Agadi, kutsidya la kum’mawa kwa Yorodano.+
19 Akazi anu okha ndi ana anu aang’ono ndiwo atsale m’mizinda yanu imene ndakupatsani.+ Ziweto zanunso zitsale (ndikudziwa kuti muli ndi ziweto zambiri),
8 Kenako tinatenga dziko lawo ndi kulipereka monga cholowa kwa fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase.+
8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa Arubeni ndi kwa Agadi, kutsidya la kum’mawa kwa Yorodano.+