Yoswa 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mukakangoti mwalanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezo malinga ndi mawu a Yehova. Izi n’zimene ndakulamulani.”+
8 Ndipo mukakangoti mwalanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezo malinga ndi mawu a Yehova. Izi n’zimene ndakulamulani.”+