Miyambo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Madalitso amapita pamutu pa wolungama,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+