Genesis 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo iye anati: “Ndikutemberera Kanani.+ Akhale kapolo wapansi kwambiri kwa abale ake.”+ Genesis 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anawonjezera kuti:“Adalitsike Yehova,+ Mulungu wa Semu,Ndipo Kanani akhale kapolo kwa iye.+