Genesis 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara. Numeri 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe.
2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara.
22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe.