Deuteronomo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kwera pamwamba pa Pisiga+ ndi kukweza maso ako, ndipo uyang’ane kumadzulo, kumpoto, kum’mwera ndi kum’mawa, uone dzikolo ndi maso ako, chifukwa suwoloka Yorodano uyu.+
27 Kwera pamwamba pa Pisiga+ ndi kukweza maso ako, ndipo uyang’ane kumadzulo, kumpoto, kum’mwera ndi kum’mawa, uone dzikolo ndi maso ako, chifukwa suwoloka Yorodano uyu.+