Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+