Yoswa 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pomaliza, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye, anatembenuka n’kupita kumzinda wa Debiri,+ n’kuyamba kuuthira nkhondo.
38 Pomaliza, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye, anatembenuka n’kupita kumzinda wa Debiri,+ n’kuyamba kuuthira nkhondo.