Aefeso 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,”+ ndilo lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo:+