Yoswa 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yabini mfumu ya ku Hazori+ atangomva nkhaniyi, anatumiza uthenga woitanitsa Yobabi mfumu ya ku Madoni, ndi mfumu ya ku Simironi, ndiponso mfumu ya ku Akasafu.+
11 Ndiyeno Yabini mfumu ya ku Hazori+ atangomva nkhaniyi, anatumiza uthenga woitanitsa Yobabi mfumu ya ku Madoni, ndi mfumu ya ku Simironi, ndiponso mfumu ya ku Akasafu.+