1 Mbiri 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ana a Gadi+ omwe anali pafupi nawo, anali kukhala m’dziko la Basana+ mpaka ku Saleka.+