Yoswa 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Malirewo anapitirira mpaka kumalo otsetsereka a kumpoto kwa Beti-hogila,+ n’kukathera kugombe la kumpoto kwa Nyanja Yamchere,+ kumapeto a kum’mwera a mtsinje wa Yorodano. Awa anali malire a kum’mwera a gawo la Benjamini.
19 Malirewo anapitirira mpaka kumalo otsetsereka a kumpoto kwa Beti-hogila,+ n’kukathera kugombe la kumpoto kwa Nyanja Yamchere,+ kumapeto a kum’mwera a mtsinje wa Yorodano. Awa anali malire a kum’mwera a gawo la Benjamini.