Yoswa 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Analowera chakumpoto n’kukafika ku Eni-semesi mpaka ku Gelilotu, yemwe ali kutsogolo kwa chitunda cha Adumi.+ Kuchokera pamenepo, anatsetserekera kumwala+ wa Bohani,+ mwana wa Rubeni.
17 Analowera chakumpoto n’kukafika ku Eni-semesi mpaka ku Gelilotu, yemwe ali kutsogolo kwa chitunda cha Adumi.+ Kuchokera pamenepo, anatsetserekera kumwala+ wa Bohani,+ mwana wa Rubeni.