Yoswa 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Malire a kum’mwera a gawolo anayambira kumapeto kwa Kiriyati-yearimu, n’kulowera chakumadzulo, n’kupitirira kukafika kukasupe wa madzi a Nafitoa.+
15 Malire a kum’mwera a gawolo anayambira kumapeto kwa Kiriyati-yearimu, n’kulowera chakumadzulo, n’kupitirira kukafika kukasupe wa madzi a Nafitoa.+