Oweruza 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno zinachitika kuti pamene Akisa anali kupita kunyumba, anali kulimbikitsa Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anawomba m’manja ali pabulu.*+ Atatero, Kalebe anamufunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”
14 Ndiyeno zinachitika kuti pamene Akisa anali kupita kunyumba, anali kulimbikitsa Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anawomba m’manja ali pabulu.*+ Atatero, Kalebe anamufunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”