Oweruza 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno a fuko la Yuda anauza abale awo a fuko la Simiyoni kuti: “Tiyeni tipitire limodzi m’gawo la fuko lathu+ kuti tikamenyane ndi Akanani. Kenako ifenso tidzapita nanu kugawo lanu.”+ Choncho fuko la Simiyoni linapita nawo.+
3 Ndiyeno a fuko la Yuda anauza abale awo a fuko la Simiyoni kuti: “Tiyeni tipitire limodzi m’gawo la fuko lathu+ kuti tikamenyane ndi Akanani. Kenako ifenso tidzapita nanu kugawo lanu.”+ Choncho fuko la Simiyoni linapita nawo.+