Yoswa 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kuchokera m’fuko la Aseri,+ anawapatsa Misali+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Abidoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mbiri 6:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Kuchokera ku fuko la Aseri anawapatsa mzinda wa Masala ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Abidoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
30 Kuchokera m’fuko la Aseri,+ anawapatsa Misali+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Abidoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
74 Kuchokera ku fuko la Aseri anawapatsa mzinda wa Masala ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Abidoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto,