Numeri 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wakupha munthuyo ayenera kukhala mumzinda wothawirako kufikira mkulu wa ansembe atamwalira.+ Pambuyo pa imfa ya mkulu wa ansembe, wakupha munthuyo ayenera kubwerera kumalo a cholowa chake.
28 Wakupha munthuyo ayenera kukhala mumzinda wothawirako kufikira mkulu wa ansembe atamwalira.+ Pambuyo pa imfa ya mkulu wa ansembe, wakupha munthuyo ayenera kubwerera kumalo a cholowa chake.