Oweruza 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo mwini nyumbayo anatuluka ndi kuwauza kuti:+ “Iyayi abale anga,+ chonde, musachite choipa chilichonse, chifukwa munthuyu wabwera m’nyumba yanga. Musachite chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi ngati chimenechi.+
23 Pamenepo mwini nyumbayo anatuluka ndi kuwauza kuti:+ “Iyayi abale anga,+ chonde, musachite choipa chilichonse, chifukwa munthuyu wabwera m’nyumba yanga. Musachite chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi ngati chimenechi.+